Pitani ku nkhani yake

BAIBULO LIMASINTHA ANTHU

Ndinasiya Kupita Kuchipembedzo Chilichonse

Ndinasiya Kupita Kuchipembedzo Chilichonse

Tom ankafunitsitsa kuti azikhulupirira Mulungu koma anakhumudwa ndi zochita za chipembedzo. Onerani vidiyoyi kuti muone mmene kuphunzira Baibulo kunamuthandizira kuti akhale ndi chiyembekezo.