Pitani ku nkhani yake

Kugwira Ntchito ndi a Mboni za Yehova

Kugwira Ntchito ndi a Mboni za Yehova

Kodi munayamba mwaganizirapo mmene zimakhalira pogwira ntchito zomangamanga limodzi ndi a Mboni za Yehova? Tamvani zimene makontilakitala ena ananena.