Pitani ku nkhani yake

Pitani ku menyu yachiwiri

Mboni za Yehova

Chichewa

Mwambo wa Omaliza Maphunziro ku Giliyadi, Kalasi Nambala 136

Mwambo wa Omaliza Maphunziro ku Giliyadi, Kalasi Nambala 136

Anthu amene anamaliza maphunziro ku sukulu ya Giliyadi amatumizidwa kuti akalimbikitse abale ndi alongo awo padziko lonse. Mvetserani zimene ena akufotokoza zokhudza zimene anachita podzipereka ndi mtima wonse.