Anthu 1.4 miliyoni a m’mayiko osiyanasiyana anamvetsera msonkhano wapachaka wa nambala 129, wa bungwe la Watch Tower Bible and Tract Society of Pennsylvania kudzera pa vidiyo ya pa Intaneti. Msonkhanowu umachitika kamodzi chaka chilichonse. Onerani zimene zinachitika pa msonkhano wosangalatsawu.