Pitani ku nkhani yake

Zimene Zinachitika pa Msonkhano Wapachaka wa 2014

Zimene Zinachitika pa Msonkhano Wapachaka wa 2014

Anthu ochokera m’mayiko osiyanasiyana anapezeka pa msonkhano wa nambala 130 umene Bungwe la Watch Tower Bible and Tract Society of Pennsylvania limachita chaka chilichonse. Onerani zimene zinachitika pa msonkhano wosaiwalikawu.

Mukhoza kuwonera pulogalamu yonse ya Msonkhano Wapachaka wa 2014 pa TV ya JW.