Crystal, yemwe ankachitidwa nkhanza zokhudza kugonana ali wamng’ono akufotokoza mmene kuphunzira Baibulo kunamuthandizira kuti akhale paubwenzi ndi Yehova ndiponso kudziwa kuti moyo wake ndi wofunika kwambiri.