Lemba lina la m’Baibulo linathandiza kwambiri Hércules kuzindikira kuti akhoza kusintha khalidwe lake lankhanza n’kukhala munthu wabwino.