M’mwezi wa June 2013, a Mboni za Yehova anathandiza anthu amene anakhudzidwa ndi madzi osefukira ku Canada. Onerani vidiyoyi kuti mudziwe zimene a Mboniwa anachita.