Pitani ku nkhani yake

Muziteteza Ana Anu

Muziteteza Ana Anu

Vidiyoyi inatulutsidwa ndi Mboni za Yehova m’Chingelezi ndi m’Chisipanishi chaka cha 2002 ndipo ikusonyeza mmene makolo athandizidwira kupeza njira zotetezera ana awo kwa anthu ogona ndi ana.