Kuthandiza Ena

KUTHANDIZA ENA

Kuthandiza Anthu Omwe Ali ndi Vuto Losamva ku Indonesia

Anthu a vuto losamva akuthandizidwa chifukwa chophunzira Baibulo ku Indonesia.

KUTHANDIZA ENA

Kuthandiza Anthu Omwe Ali ndi Vuto Losamva ku Indonesia

Anthu a vuto losamva akuthandizidwa chifukwa chophunzira Baibulo ku Indonesia.

Kutonthoza Komanso Kuthandiza Anthu Omwe Akudwala

Kodi a Mboni za Yehova amasonyeza bwanji chikondi kwa a Mboni anzawo omwe akudwala kwambiri?

Aphunzitsi ku Philippines Anaona Kuti Webusaiti ya JW.ORG Ndi Yothandiza

Kodi aphunzitsi oposa 1,000 komanso olangiza ana anaphunzira chiyani zokhudza webusaitiyi?

Kodi Nyumba ya Ufumu Ingathandize Bwanji Anthu M’dera Lanu?

Werengani nkhaniyi kuti mumve zimene anthu ena ananena Nyumba ya Ufumu itamangidwa m’dera lawo.

A Mboni ku Italy Anathandiza Anthu a M’dera Lawo

Kodi anthu ankafunikira kuthandizidwa motani? A Mboni anathandiza bwanji?

Ntchito Imene Inathandiza Anthu Kuti Asadziphe

N’chifukwa chiyani a Mboni za Yehova anakonza zoti kwa miyezi iwiri agwire ntchito yapadera yolalikira m’dera la Tabasco ku Mexico? Kodi ntchitoyi inathandiza bwanji anthu?

A Mboni za Yehova Anathandiza Pantchito Yoyeretsa Nkhalango Pafupi ndi Mzinda wa Lviv

N’chifukwa chiyani iwo anathandiza anthu a m’dera lawo m’njira imeneyi?

A Mboni Akulimbikitsa ndi Kutonthoza Okalamba

A Mboni za Yehova amayendera okalamba omwe ali kunyumba zosungira okalamba ku Australia.

A Mboni za Yehova Analimbikitsa Anthu ku France

A Mboni za Yehova anaika timashelefu ta mabuku m’malo osiyanasiyana ku mpikisano wa njinga wa ku France pofuna kuuza anthu uthenga wolimbikitsa komanso wotonthoza.

Kuthandiza Anthu Othawa Kwawo Omwe Ali ku Central Europe

Anthu othawa kwawo amafunikanso kuwalimbikitsa osati kungowapatsa chakudya ndi malo okhala basi. A Mboni ongodzipereka akulimbikitsa anthu ndi uthenga wa m’Baibulo komanso kuwathandiza kukhala ndi chiyembekezo.

A Mboni za Yehova Anagwira Ntchito Yosesa Mumzinda wa Rostov-on-Don

Akuluakulu a mumzinda wa Rostov-on-Don ku Russia, analemba kalata yoyamikira a Mboni za Yehova chifukwa chogwira nawo ntchito yosesa mumzindawo.

A Mboni Anathandiza Ana Ena ku Thailand Kuti Zinthu Ziziwayendera Bwino Kusukulu

A Mboni za Yehova ku Thailand anagwira ntchito yapadera yothandiza ana a sukulu kuti zinthu ziziwayendera bwino kusukulu. Kodi akuluakulu a m’sukuluzi, aphunzitsi komanso makolo ananena zotani?

A Mboni za Yehova a ku Hungary Anayamikiridwa Chifukwa Chothandiza Kuti Madzi Asasefukire

Mtsinje wa Danube unadzaza kwambiri ndipo kanali koyamba kuti udzaze choncho. A Mboni za Yehova anagwira nawo ntchito yoteteza kuti mtsinjewu usasefukire yomwe inakonzedwa ndi akuluakulu a m’dzikolo.

Wozimitsa Moto Yemwe Anali Patchuthi Anapulumutsa Anthu

A Serge Gerardin omwe ndi a Mboni za Yehova ndipo amagwira ntchito yozimitsa moto ku France, anathandiza mwachangu pa ngozi ndipo anapulumutsa anthu.

A Mboni za Yehova Analandira Ulemu Chifukwa Chothandiza Akaidi

A Mboni za Yehova anagwira ntchito yofunika kwambiri yothandiza akaidi m’dziko la Australia kumalo ena aakulu kwambiri osungirako anthu olowa m’dzikolo mopanda chilolezo. Kodi ntchito yake mukuidziwa?

Webusaiti ya JW.ORG Ikuthandiza Anthu Kwambiri

Anthu osiyanasiyana akunena mmene malangizo ochokera m’Baibulo opezeka pa jw.org akuwathandizira.

A Mboni za Yehova Amaphunzitsa Makolo ndi Ana Mmene Angapewere Anthu Ogwiririra Ana

Kwa zaka zambiri, a Mboni za Yehova akhala akulemba komanso kufalitsa nkhani zimene zimathandiza kuti aliyense azisangalala m’banja.

Kuthana ndi Tsankho Pogwiritsa Ntchito Baibulo

A Mboni za Yehova amakhulupirira zoti Mulungu amaona kuti mitundu yonse ya anthu ndi yofanana.

Chikhulupiriro Chinathandiza Kwambiri Anthu Omwe Anakhudzidwa ndi Mvula Yamkuntho ku Philippines

Anthu opulumuka akufotokoza zimene zinachitika pa nthawi ya mvula yamkuntho ya Haiyan.

Madzi Osefukira ku Alberta

Kodi a Mboni za Yehova anathandiza bwanji anthu amene anakhudzidwa ndi madzi osefukira m’dera la Alberta ku Canada?

Zinthu Zinayamba Kuyenda Bwino

Donald, yemwe m’mbuyomo anamangidwa, anafotokoza mmene kuphunzira Baibulo kunamuthandizira kuti adziwe Mulungu, asinthe moyo wake komanso kuti azikonda kwambiri mkazi wake.

Bukhu la Nkhani za Baibulo Layamba Kugwiritsidwa Ntchito Kusukulu

Bukhu Langa la Nkhani za Baibulo la m’Chipangasinani, limene likufalitsidwa ndi a Mboni za Yehova, likuthandiza ana a sukulu ambirimbiri ku Philippines. Zimenezi zikuchitika motani?

Munthu Wina Anapulumutsidwa Akufuna Kudzipha Pansanja ya Sky Tower

Bambo wa zaka 80 yemwe ndi wa Mboni za Yehova anathandiza munthu wina yemwe ankafuna kudumpha pansanja ya Sky Tower ku Auckland m’dziko la New Zealand.

A Mboni za Yehova Analandira Satifiketi Yaulemu Chifukwa Choteteza Chilengedwe

Fakitale ya Mboni za Yehova yosindikiza mabuku ku Mexico yakhala ikulandira satifiketi yaulemu kwa zaka 7 zotsatizana chifukwa choteteza chilengedwe.

Anthu Akuthandizidwa Kusintha Moyo Wawo: Mkaidi Anasintha

Ku Spain, a Mboni za Yehova akuphunzira Baibulo ndi akaidi pafupifupi 600. Werengani nkhaniyi kuti muone mmene zimenezi zinathandizira mkaidi kusintha moyo wake.

Pa Nthawi ya Tsoka, Timathandizana Chifukwa cha Chikondi

M’mayiko ambirimbiri, a Mboni za Yehova amathandiza anthu amene ali m’mavuto.

Anapulumutsidwa Akufuna Kudzipha

Nkhani zenizeni zochitika m’mayiko osiyanasiyana padziko lapansili zosonyeza mmene anthu ena anathandizidwira kuti asadziphe.

“Ndinu Anthu Achitsanzo Chabwino Kwambiri”

Madzi osefukira pamodzi ndi matope atawononga mzinda wa Saponara ku Italy, gulu la anthu ongodzipereka linagwira ntchito mwakhama yokonza zinthu zimene zinawonongeka.

Anthu Ambiri Aphunzira Kuwerenga ndi Kulemba

Werengani zimene anthu ochokera m’mayiko osiyanasiyana ananena zokhudza mmene sukulu yophunzitsa kuwerenga ndi kulemba ya a Mboni za Yehova yawathandizira.

A Mboni za Yehova Akuthandiza Anthu a Kundende ndi Mawu a Mulungu

Kodi a Mboni za Yehova akuchita zotani pofuna kuthandiza anthu amene ali m’ndende?