Pitani ku nkhani yake

Webusaiti ya JW.ORG Ikuthandiza Anthu Kumva Uthenga wa M’Baibulo

Webusaiti ya JW.ORG Ikuthandiza Anthu Kumva Uthenga wa M’Baibulo

Pa August 28, 2012, a Mboni za Yehova anatsegula webusaiti ya jw.org ataikonzanso. Onani mmene webusaitiyi ikuthandizira anthu a Mboni komanso omwe si a Mboni.