Pitani ku nkhani yake

Tapatsidwa Ntchito Yomasulira “Mawu Opatulika a Mulungu”​—Aroma 3:2

Tapatsidwa Ntchito Yomasulira “Mawu Opatulika a Mulungu”​—Aroma 3:2

Mfundo zoona zochokera kwa Mulungu zikhoza kupezeka m’Mabaibulo osiyanasiyana, ndipo a Mboni za Yehova akhala akugwiritsira ntchito Mabaibulo ambirimbiri kwa zaka zochuluka. Koma n’chifukwa chiyani a Mboni anaganiza zomasulira okha Baibulo m’Chingelezi chimene anthu amalankhula masiku ano, ndipo zotsatira zake n’zotani? Onerani vidiyo yakuti, Tapatsidwa Ntchito Yomasulira “Mawu Opatulika a Mulungu”​—Aroma 3:2.