Onerani vidiyoyi kuti mudziwe zokhudza gulu la anthu ongodzipereka ochokera m’madera osiyanasiyana padziko lapansili amene amabwera kudzaimba nyimbo.