Onani chuma cha Akhristu a Mboni za Yehova chomwe ndi zinthu zakale zamtengo wapatali. Chumachi chili kumalo awo osonyeza zinthu zakale omwe ali ku likulu lawo lapadziko lonse ku Brooklyn, New York.