Pitani ku nkhani yake

Moyo wa pa Beteli

MOYO WA PA BETELI

Anakwanitsa Kuzimitsa Moto

Ubwino wophunzira kuzimitsa moto unaoneka moto utabuka.

MOYO WA PA BETELI

Anakwanitsa Kuzimitsa Moto

Ubwino wophunzira kuzimitsa moto unaoneka moto utabuka.

Tikukuitanani Kuti Mudzaone Maofesi Athu ku United States

Mudzaonanso Likulu la Padziko Lonse la Mboni za Yehova lomwe lili ku United States.

Kodi Kuofesi ya Mboni za Yehova Kumachitika Zotani?

Alendo amaloledwa kudzaona maofesi athu. Tikukupemphani kuti inunso mupite kukaona zimene zimachitika kumeneko!

Anthu Ambiri Anakaona Ofesi ya Nthambi ya Central America

Kwa anthu ena, sizinali zophweka kuti apite kukaona ofesi ya nthambi. Ambiri anayenda kwa masiku angapo pa mabasi omwe anapanga hayala. Kodi ana komanso achinyamata ananena chiyani atapita kukaona Beteli?

Chionetsero cha Baibulo Cholemekeza Dzina la Mulungu

Malowa anatsegulidwa mu 2013, kumalikulu anthu apadziko lonse. Mabaibulo amene anaperekedwa anali akale kwambiri.

Chionetsero Chapadera cha Baibulo

Kuyambira kale, Yehova Mulungu wakhala akuuza anthu dzina lake. Onerani vidiyoyi kuti mudziwe zimene omasulira Baibulo achita pofuna kuti dzina la Mulungu lisaiwalike.

Tsiku Lapadera Lokaona Malo ku Steinfels

Ofesi ya Mboni za Yehova ya ku Central Europe inaitana anthu okhala pafupi, abizinezi ndiponso akukuakulu a boma kuti adzaone maofesiwa. Tsiku lapaderali linali ndi mutu wakuti: “Takwanitsa Zaka 30 Tili ku Selters Kuno.” Kodi ena mwa anthu 3,000 omwe anapita kumalowa ananena zotani?

Ulendo Wosaiwalika

Bambo Marcellus analimbana ndi mavuto ambiri kuti ulendo wawo okaona ofesi ya nthambi ya ku United States ndiponso malikulu apadziko lonse a Mboni za Yehova utheke. Kodi ulendowu unalidi wofunikadi?

Patha Zaka 50 Tili ku Wallkill

Muvidiyoyi, Bambo George Couch akufotokoza mbiri yokhudza mmene a Mboni za Yehova anapezera famu yachiwiri, imene imadziwika ndi dzina lakuti Watchtower Farms, yomwe ili pafupi ndi mzinda wa New York City.

Kusamuka ku 117 Adams Street

Anthu a m’banja la Beteli akufotokoza zokhudza ntchito yofunika kwambiri yosindikiza mabuku imene inkachitika ku Brooklyn.

Tisamuke Pasanathe Masiku 60!

A Mboni za Yehova anasamuka m’nyumba zokwana 5. Malo onse a mkati mwa nyumbazi, kukula kwake n’kofanana ndi mabwalo a mpira okwana 11. Kodi gulu la ogwira ntchito amenewa linakwanitsa bwanji kusamuka pamasiku amene anakonza?

Chikwangwani Chakalekale

Onerani kuti mudziwe zambiri zokhudza chikwangwani cha Watchtower, chomwe ndi chotchuka kwambiri ku Brooklyn, New York.

Mafamu a Watchtower Akhala Akuthandiza Kwambiri kwa Zaka 50

Werengani nkhaniyi kuti mudziwe mmene famuyi yasinthira kwa zaka zambiri kuti ithandize pa ntchito ya padziko lonse yophunzitsa anthu Baibulo imene a Mboni za Yehova amachita.

Famu Yomwe Ikudyetsa Anthu Mamiliyoni

Werengani nkhaniyi kuti mudziwe mmene malo athu osindikizira mabuku amene ali kufamu ya Watchtower kumpoto kwa dera la New York, akuthandizira anthu mamiliyoni kuti azidya chakudya chauzimu.

Ophunzira a pa Yunivesite Ina Anakaona Ofesi ya Nthambi ya Mboni za Yehova ku Mexico

Ophunzira a pa yunivesite yotchedwa National School of Library and Archival Sciences anakaona ofesi yathu ku Mexico. Wophunzira m’modzi anaona kuti ulendowu unamuthandiza kusiya tsankho.

Kulondile ya pa Beteli Amachapa Chilichonse

Achinyamata amene ali pamaofesi a Mboni za Yehova ku United States anadzipereka kuti azigwira ntchito yochapa zovala zolemera matani 1,800 chaka chilichonse.

Nthawi Yochoka ku Hotelo ya Bossert ku Brooklyn Mumzinda wa New York

A Mboni za Yehova anagulitsa nyumba yomwe inali ya nsanja 14 yomangidwa ngati nyumba za ku Italy za m’zaka za m’ma 1500 kapena 1600. Werengani nkhaniyi kuti mudziwe zambiri zokhudza nyumba yokongolayi yomwe yakhala zaka zoposa 100.