Pitani ku nkhani yake

Pemphani Kuti Munthu Akuyendereni

Kodi mukufuna kudziwa zambiri zokhudza Baibulo kapena a Mboni za Yehova? Ngati mukufuna, pemphani kuti wa Mboni za Yehova akuyendereni polemba fomu ili m’munsimu ndipo wa Mboni m’dera lanu adzalankhula nanu.

Tidzagwiritsa ntchito zomwe mwatumiza poyankha pempho lanu ndipo sitidzazigwiritsa ntchito pa zinthu zina. Zimenezi n’zogwirizana ndi mfundo zathu zopezeka mu Global Policy on Use of Personal Data.

Chidziwitso Chokhudza Matenda a Kolonavairasi (COVID-19): M’madera ambiri tasiya kaye kukumana ndi anthu pamasom’pamaso komanso kusonkhana malo amodzi. Mukamalemba fomuyi, chonde ikani nambala yanu ya foni ndipo wa Mboni wa m’dera lanu adzakuimbirani.