Zokhudza screen reader

Sankhani chinenero

Pitani ku menyu yachiwiri

Pitani ku nkhani yake

Mboni za Yehova

Chichewa

Zina Zomwe Zili M’mavidiyo a Msonkhano Wachigawo wa 2016

Zina Zomwe Zili M’mavidiyo a Msonkhano Wachigawo wa 2016

Onerani zina zomwe zili m’mavidiyo awiri a msonkhano wachigawo wa Mboni za Yehova wa 2016. Tidzakulandirani ku chigawo chilichonse cha msonkhanowu. Simudzalipiritsidwa ndalama iliyonse ndipo sikudzayendetsedwa mbale iliyonse yotolera ndalama.