Pitani ku nkhani yake

Pitani ku menyu yachiwiri

Mboni za Yehova

Chichewa

Misonkhano Yathu Yapachaka

Misonkhano Yathu Yapachaka

Kachigawo ka vidiyo kano kachokera mu DVD yakuti, Mboni za Yehova—Gulu Limene Likulalikira Uthenga Wabwino, yofalitsidwa ndi Mboni za Yehova.

Onaninso

KODI NDANI AKUCHITA CHIFUNIRO CHA YEHOVA MASIKU ANO?

N’chifukwa Chiyani a Mboni za Yehova Amakhala ndi Misonkhano Ikuluikulu?

Chaka chilichonse, timachita misonkhano ikuluikulu. Kodi kupezeka pamisonkhano imeneyi kungakuthandizeni bwanji?

KODI NDANI AKUCHITA CHIFUNIRO CHA YEHOVA MASIKU ANO?

Kodi a Mboni za Yehova ndi Anthu Otani?

Kodi ndi anthu angati a Mboni za Yehova amene inuyo mumawadziwa? Kodi mumadziwa zotani zokhudza anthuwo?