Pitani ku nkhani yake

Pitani ku menyu yachiwiri

Mboni za Yehova

Chichewa

Tikukuitanani Kuti Mudzakhale Nafe Pamsonkhano

Tikukuitanani Kuti Mudzakhale Nafe Pamsonkhano

Anthu ambiri masiku ano ndi okhumudwa. Koma Baibulo limatiuza kuti ‘Musafooke.’ Msonkhano wa Mboni za Yehova wa chaka chino, ufotokoza mmene tingakhalire osangalala panopa komanso mmene tingadzakhalire moyo wabwino m’tsogolo.