Pitani ku nkhani yake

Pitani ku menyu yachiwiri

Mboni za Yehova

Chichewa

Mfundo Zokhudza Maofesi Ndiponso Kuona Malo

Tikukuitanani kuti mudzaone maofesi athu komanso malo athu osindikizira mabuku ndipo tidzakulandirani ndi manja awiri. Dziwani malo amene kuli maofesiwa komanso nthawi imene mungaone malo.

 

Zambia

Farm 23 A Makeni Road

Opposite Makeni Police Station

10101 LUSAKA

ZAMBIA

+260 21-1-272-062

Kuona Malo

Lolemba mpaka Lachisanu

8:00 a.m. mpaka 11:00 a.m. ndi 1:00 p.m. mpaka 3:30 p.m.

Nthawi yonse: Mphindi 50

Zimene Timachita

Timamasulira mabuku ofotokoza nkhani za m’Baibulo m’zinenero 14. Timatumiza mabuku kumipingo yoposa ??? ya Mboni za Yehova ku Zambia.

Koperani pepala losonyeza ofesi yathu.