Pitani ku nkhani yake

Pitani ku menyu yachiwiri

Mboni za Yehova

Chichewa

Mfundo Zokhudza Maofesi Ndiponso Kuona Malo

Tikukuitanani kuti mudzaone maofesi athu komanso malo athu osindikizira mabuku ndipo tidzakulandirani ndi manja awiri. Dziwani malo amene kuli maofesiwa komanso nthawi imene mungaone malo.

 

United States

Brooklyn

25 Columbia Heights

BROOKLYN NY 11201-2483

UNITED STATES

+1 718-560-5000

Kuona Zithunzi Zimene Zili Pamalo Ofikira Alendo

Lolemba mpaka Lachisanu

8:00 a.m. mpaka 5:00 p.m.

Nthawi yonse: Maola awiri

DZIWANI IZI: Panopa gulu laimitsa kaye ntchito yoonetsa anthu malo ku Brooklyn chifukwa cha ntchito yokonzekera kusamutsa likulu la Mboni za Yehova kupita ku Warwick, New York. Tsiku lomaliza limene anthu akhoza kukaona zithunzi zimene zili pamalo ofikira alendo ndi pa 15 July 2016.

Zimene Timachita

Timayang’anira ntchito imene Mboni za Yehova zikugwira padziko lonse. Alendo odzaona malo amasonyezedwanso zinthu zina za mbiri yakale zosonyeza mmene ntchito yathu yakulira masiku ano.

Patterson

100 Watchtower Dr. (2891 Route 22)

PATTERSON NY 12563

UNITED STATES

+1 845-306-1000

Kuona Malo

Lolemba mpaka Lachisanu

8:00 a.m. mpaka 11:00 a.m. ndi 1:00 p.m. mpaka 4:00 p.m.

Nthawi yonse: Ola limodzi ndi hafu

Zimene Timachita

Timajambula zithunzi zimene timazigwiritsa ntchito m’mabuku athu komanso mavidiyo ndi zinthu zina zomvetsera. Timamasulira mabuku ofotokoza nkhani za m’Baibulo m’Chinenero Chamanja cha ku America. Alendo odzaona malo amauzidwanso za masukulu osiyanasiyana ophunzitsa Baibulo amene ali kuno.

Wallkill

900 Red Mills Rd.

WALLKILL NY 12589

UNITED STATES

+1 845-744-6000

Kuona Malo

Lolemba mpaka Lachisanu

8:00 a.m. mpaka 11:00 a.m. ndi 1:00 p.m. mpaka 4:00 p.m.

Nthawi yonse: Maola awiri ndi hafu

Zimene Timachita

Chaka chilichonse timasindikiza mabuku ofotokoza nkhani za m’Baibulo oposa 25 miliyoni. Timatumizanso mabuku a m’zinenero zoposa 360 kumaofesi athu ena padziko lonse komanso kumipingo yoposa 15,000 ya Mboni za Yehova ku United States, Canada ndi ku Caribbean.

Koperani pepala losonyeza ofesi yathu.