Pitani ku nkhani yake

Mfundo Zokhudza Maofesi Ndiponso Kuona Malo

Tikukuitanani kuti mudzaone maofesi athu komanso malo athu osindikizira mabuku ndipo tidzakulandirani ndi manja awiri. Dziwani malo amene kuli maofesiwa komanso nthawi imene mungaone malo.

 

Ukraine

Lvivska Street 64

Briukhovychi

79491 LVIV

UKRAINE

+38 032-240-9200

Kuona Malo

Lolemba mpaka Lachisanu

8:00 a.m. mpaka 10:30 a.m. ndi 1:00 p.m. mpaka 3:00 p.m.

Nthawi yonse: Ola limodzi ndi hafu

Zimene Timachita

Timayang’anira ntchito yophunzitsa anthu Baibulo ku Ukraine imene mipingo yoposa 1,700 ya Mboni za Yehova ikugwira komanso ntchito yomanga Nyumba za Ufumu m’dzikoli. Timamasulira mabuku ofotokoza nkhani za m’Baibulo m’Chiyukireniya.

Koperani pepala losonyeza ofesi yathu.