Pitani ku nkhani yake

Mfundo Zokhudza Maofesi Ndiponso Kuona Malo

Tikukuitanani kuti mudzaone maofesi athu komanso malo athu osindikizira mabuku ndipo tidzakulandirani ndi manja awiri. Dziwani malo amene kuli maofesiwa komanso nthawi imene mungaone malo.

 

Taiwan

Watch Tower Bible and Tract Society

3-12, Shetze Village

HSINWU 32746

TAIWAN

+886 3-477-7999

Kuona Malo

Lolemba mpaka Lachisanu

8:00 a.m. mpaka 11:00 a.m. ndi 1:00 p.m. mpaka 4:00 p.m.

Nthawi yonse: Ola limodzi

Zimene Timachita

Timajambula zinthu zomvetsera m’Chitchainizi cha Mandarini. Timamasulira mabuku ofotokoza nkhani za m’Baibulo m’Chinenero Chamanja cha ku Taiwan.

Koperani pepala losonyeza ofesi yathu.