Pitani ku nkhani yake

Mfundo Zokhudza Maofesi Ndiponso Kuona Malo

Tikukuitanani kuti mudzaone maofesi athu komanso malo athu osindikizira mabuku ndipo tidzakulandirani ndi manja awiri. Dziwani malo amene kuli maofesiwa komanso nthawi imene mungaone malo.

 

Tahiti

P.K. 2,7 Cote mer

Toahotu

Taiarapu Ouest

TARAVAO TAHITI

FRENCH POLYNESIA

+689 40-54-70-00

Kuona Malo

Lolemba mpaka Lachisanu

8:00 a.m. mpaka 11:00 a.m. ndi 1:00 p.m. mpaka 4:00 p.m.

Nthawi yonse: Ola limodzi ndi hafu

Zimene Timachita

Timamasulira mabuku ototokoza nkhani za m’Baibulo m’Chitahiti. Timayang’anira ntchito yophunzitsa anthu Baibulo imene Mboni za Yehova zikugwira pazilumba zambiri zomwe zili m’dera lalikulu mofanana ndi chigawo cha Western Europe.

Koperani pepala losonyeza ofesi yathu.