Pitani ku nkhani yake

Pitani ku menyu yachiwiri

Mboni za Yehova

Chichewa

Mfundo Zokhudza Maofesi Ndiponso Kuona Malo

Tikukuitanani kuti mudzaone maofesi athu komanso malo athu osindikizira mabuku ndipo tidzakulandirani ndi manja awiri. Dziwani malo amene kuli maofesiwa komanso nthawi imene mungaone malo.

 

Suriname

Garnizoenspad 239

DISTRICT WANICA

SURINAME

+597 328054

+597 328049

+597 328021

+597 328019

Kuona Malo

Lolemba mpaka Lachisanu

8:00 a.m. mpaka 11:00 a.m. ndi 1:00 p.m. mpaka 4:00 p.m.

Nthawi yonse: Mphindi 45

Zimene Timachita

Timayang’anira ntchito imene Mboni za Yehova zikugwira ku Suriname. Timamasulira mabuku ofotokoza nkhani za m’Baibulo m’zinenero zisanu, kuphatikizapo Chinenero Chamanja cha ku Suriname. Timajambulanso zinthu zina zomvetsera m’zinenero zinanso zingapo.

Koperani pepala losonyeza ofesi yathu.