Pitani ku nkhani yake

Pitani ku menyu yachiwiri

Mboni za Yehova

Chichewa

Mfundo Zokhudza Maofesi Ndiponso Kuona Malo

Tikukuitanani kuti mudzaone maofesi athu komanso malo athu osindikizira mabuku ndipo tidzakulandirani ndi manja awiri. Dziwani malo amene kuli maofesiwa komanso nthawi imene mungaone malo.

 

Sri Lanka

Watch Tower Bible and Tract Society of Lanka

711 Station Road

WATTALA 11300

SRI LANKA

+94 11-2930-444

Kuona Malo

Lolemba mpaka Lachisanu

8:00 a.m. mpaka 11:15 a.m. ndi 1:00 p.m. mpaka 4:00 p.m.

Nthawi yonse: Mphindi 45

Zimene Timachita

Timamasulira mabuku ofotokoza nkhani za m’Baibulo m’Chisinihala. Timajambulanso zinthu zina zomvetsera m’Chisinihala.

Koperani pepala losonyeza ofesi yathu.