Pitani ku nkhani yake

Mfundo Zokhudza Maofesi Ndiponso Kuona Malo

Tikukuitanani kuti mudzaone maofesi athu komanso malo athu osindikizira mabuku ndipo tidzakulandirani ndi manja awiri. Dziwani malo amene kuli maofesiwa komanso nthawi imene mungaone malo.

 

Spain

Testigos Cristianos de Jehová

Ctra. M-108 Torrejón-Ajalvir, km. 5

28864 AJALVIR (MADRID)

SPAIN

+34 918-879-700

Kuona Malo

Lolemba mpaka Lachisanu

8:30 a.m. mpaka 12:00 p.m. ndi 2:30 p.m. mpaka 4:30 p.m.

Nthawi yonse: Ola limodzi

Zimene Timachita

Timamasulira mabuku ofotokoza nkhani za m’Baibulo m’Chikatalani ndiponso m’Chinenero Chamanja cha ku Spain. Alendo odzaona malo amauzidwanso mbiri ya Mboni za Yehova ku Spain.

Koperani pepala losonyeza ofesi yathu.