Pitani ku nkhani yake

Mfundo Zokhudza Maofesi Ndiponso Kuona Malo

Tikukuitanani kuti mudzaone maofesi athu komanso malo athu osindikizira mabuku ndipo tidzakulandirani ndi manja awiri. Dziwani malo amene kuli maofesiwa komanso nthawi imene mungaone malo.

 

Sierra Leone

133 Wilkinson Road

FREETOWN

SIERRA LEONE

+232 76-679-072

+232 77-850-790

+232 76-679-075

Kuona Malo

Lolemba mpaka Lachisanu

9:00 a.m. mpaka 11:00 a.m. ndi 2:00 p.m. mpaka 4:00 p.m.

Nthawi yonse: Ola limodzi ndi hafu

Zimene Timachita

Timamasulira mabuku ofotokoza nkhani za m’Baibulo m’zinenero zitatu: Chikiriyo, Chikisi ndi Chimende.

Koperani pepala losonyeza ofesi yathu.