Pitani ku nkhani yake

Pitani ku menyu yachiwiri

Mboni za Yehova

Chichewa

Mfundo Zokhudza Maofesi Ndiponso Kuona Malo

Tikukuitanani kuti mudzaone maofesi athu komanso malo athu osindikizira mabuku ndipo tidzakulandirani ndi manja awiri. Dziwani malo amene kuli maofesiwa komanso nthawi imene mungaone malo.

 

Serbia

Tos̆in bunar 58-60

11080 Beograd (Zemun)

Serbia

+381 11-2196-224

+381 11-2197-109

+381 11-2615-930

Kuona Malo

Lolemba mpaka Lachisanu

8:00 a.m. mpaka 11:00 a.m. ndi 1:00 p.m. mpaka 4:00 p.m.

Nthawi yonse: Ola limodzi

Zimene Timachita

Timayang’anira ntchito imene Mboni za Yehova zikugwira ku Serbia ndi ku Montenegro. Timamasulira mabuku ofotokoza nkhani za m’Baibulo m’Chisebiya ndiponso Chinenero Chamanja cha ku Serbian.

Koperani pepala losonyeza ofesi yathu.