Pitani ku nkhani yake

Mfundo Zokhudza Maofesi Ndiponso Kuona Malo

Tikukuitanani kuti mudzaone maofesi athu komanso malo athu osindikizira mabuku ndipo tidzakulandirani ndi manja awiri. Dziwani malo amene kuli maofesiwa komanso nthawi imene mungaone malo.

 

Senegal

Parcelle 1

Zone 8

Almadies

DAKAR

SENEGAL

+221 33-820-80-00

Kuona Malo

Lachiwiri ndi Lachinayi

10:30 a.m. mpaka 12:30 p.m. ndi 3:00 p.m. mpaka 4:00 p.m.

Nthawi yonse: Ola limodzi

Zimene Timachita

Timamasulira mabuku ofotokoza nkhani za m’Baibulo m’zinenero 8 za m’mayiko anayi.

Koperani pepala losonyeza ofesi yathu.