Pitani ku nkhani yake

Pitani ku menyu yachiwiri

Mboni za Yehova

Chichewa

Mfundo Zokhudza Maofesi Ndiponso Kuona Malo

Tikukuitanani kuti mudzaone maofesi athu komanso malo athu osindikizira mabuku ndipo tidzakulandirani ndi manja awiri. Dziwani malo amene kuli maofesiwa komanso nthawi imene mungaone malo.

 

Russia

Administrative Center of JWs in Russia

Ul. Srednyaya 6

Solnechnoye, Kurortnyi Rayon

197739 ST. PETERSBURG

RUSSIA

+7 812-702-26-90

+7 812-432-95-50

Kuona Malo

Lolemba mpaka Lachisanu

8:30 a.m. mpaka 10:30 a.m. ndi 1:00 p.m. mpaka 3:00 p.m.

Nthawi yonse: Ola limodzi ndi hafu

Zimene Timachita

Timayang’anira ntchito yomasulira mabuku ofotokoza nkhani za m’Baibulo m’zinenero 33, kuphatikizapo Chinenero Chamanja cha ku Russia. Timayang’aniranso ntchito imene mipingo pafupifupi 2,500 ya Mboni za Yehova ikugwira.

Koperani pepala losonyeza ofesi yathu.