Pitani ku nkhani yake

Mfundo Zokhudza Maofesi Ndiponso Kuona Malo

Tikukuitanani kuti mudzaone maofesi athu komanso malo athu osindikizira mabuku ndipo tidzakulandirani ndi manja awiri. Dziwani malo amene kuli maofesiwa komanso nthawi imene mungaone malo.

 

Romania

Orzari Street No. 29-31

Sector 2

RO-021552 BUCUREŞTI

ROMÂNIA

+40 21-302-75-00

Kuona Malo

Lolemba mpaka Lachisanu

8:30 a.m. mpaka 11:00 a.m. ndi 1:30 p.m. mpaka 4:00 p.m.

Nthawi yonse: Ola limodzi ndi hafu

Zimene Timachita

Timayang’anira ntchito imene Mboni za Yehova zikugwira ku Romania. Timamasulira mabuku ofotokoza nkhani za m’Baibulo m’Chiromaniya. Timajambulanso zinthu zina zomvetsera m’Chiromaniya.

Koperani pepala losonyeza ofesi yathu.