Pitani ku nkhani yake

Pitani ku menyu yachiwiri

Mboni za Yehova

Chichewa

Mfundo Zokhudza Maofesi Ndiponso Kuona Malo

Tikukuitanani kuti mudzaone maofesi athu komanso malo athu osindikizira mabuku ndipo tidzakulandirani ndi manja awiri. Dziwani malo amene kuli maofesiwa komanso nthawi imene mungaone malo.

 

Portugal

Rua Conde Barão, 511

P-2649-513 ALCABIDECHE

PORTUGAL

+351 214-690-600

Kuona Malo

Lolemba mpaka Lachisanu

8:30 a.m. mpaka 11:30 a.m. ndi 1:30 p.m. mpaka 4:30 p.m.

Nthawi yonse: Ola limodzi

Zimene Timachita

Timatumiza mabuku kumipingo yoposa 700 ku Portugal, Azores, Madeira, Cape Verde, São Tomé & Príncipe. Timajambula mavidiyo ndi zinthu zina zomvetsera m’Chipwitikizi cha ku Ulaya ndiponso Chinenero Chamanja cha ku Portugal.

Koperani pepala losonyeza ofesi yathu.