Pitani ku nkhani yake

Mfundo Zokhudza Maofesi Ndiponso Kuona Malo

Tikukuitanani kuti mudzaone maofesi athu komanso malo athu osindikizira mabuku ndipo tidzakulandirani ndi manja awiri. Dziwani malo amene kuli maofesiwa komanso nthawi imene mungaone malo.

 

Poland

Strażnica Towarzystwo Biblijne i Traktatowe

ul. Warszawska 14

05-830 NADARZYN

POLAND

+48 22-739-16-00

Kuona Malo

Lolemba mpaka Lachisanu

8:00 a.m. mpaka 10:00 a.m. ndi 1:00 p.m. mpaka 3:00 p.m.

Nthawi yonse: Maola awiri

Zimene Timachita

Timamasulira mabuku ofotokoza nkhani za m’Baibulo m’Chipolishi. Alendo odzaona malo amauzidwanso mbiri ya Mboni za Yehova ku Poland.

Koperani pepala losonyeza ofesi yathu.