Pitani ku nkhani yake

Mfundo Zokhudza Maofesi Ndiponso Kuona Malo

Tikukuitanani kuti mudzaone maofesi athu komanso malo athu osindikizira mabuku ndipo tidzakulandirani ndi manja awiri. Dziwani malo amene kuli maofesiwa komanso nthawi imene mungaone malo.

 

Paraguay

Asociación Torre de Vigía de Biblias y Tratados

San Roque González 234

Ruta 1, Km. 17

B° 25 de Mayo

PY - 2560 CAPIATA

PARAGUAY

+595-21-578-698

Kuona Malo

Lolemba mpaka Lachisanu

8:00 a.m. mpaka 10:45 a.m. ndi 2:15 p.m. mpaka 4:15 p.m.

Nthawi yonse: Ola limodzi ndi mphindi 15

Zimene Timachita

Timayang’anira ntchito imene Mboni za Yehova pafupifupi 9,000 zikugwira ku Paraguay. Timamasulira mabuku ofotokoza nkhani za m’Baibulo ndi magazini m’Chigurani ndiponso m’Chinenero Chamanja cha ku Paraguay ndiponso timajambula mavidiyo ndiponso zinthu zina zomvetsera zofotokoza nkhani za m’Baibulo.

Koperani pepala losonyeza ofesi yathu.