Pitani ku nkhani yake

Mfundo Zokhudza Maofesi Ndiponso Kuona Malo

Tikukuitanani kuti mudzaone maofesi athu komanso malo athu osindikizira mabuku ndipo tidzakulandirani ndi manja awiri. Dziwani malo amene kuli maofesiwa komanso nthawi imene mungaone malo.

 

New Caledonia

236, rue Georges Lèques

Normandie

98800 NOUMEA

NEW CALEDONIA

+687 43-75-00

Kuona Malo

Lolemba mpaka Lachisanu

8:00 a.m. mpaka 11:00 a.m. ndi 1:00 p.m. mpaka 4:00 p.m.

Nthawi yonse: Mphindi 45

Zimene Timachita

Timayang’anira ntchito imene Mboni za Yehova zikugwira ku New Caledonia, Vanuatu ndi kuzilumba za Wallis ndi Futuna. Timamasulira mabuku ofotokoza nkhani za m’Baibulo m’Chiwalisi, Chilifu, Chibisilama ndiponso m’zinenero zina zisanu za m’madera amenewa.

Koperani pepala losonyeza ofesi yathu.