Pitani ku nkhani yake

Mfundo Zokhudza Maofesi Ndiponso Kuona Malo

Tikukuitanani kuti mudzaone maofesi athu komanso malo athu osindikizira mabuku ndipo tidzakulandirani ndi manja awiri. Dziwani malo amene kuli maofesiwa komanso nthawi imene mungaone malo.

 

Myanmar

94-B Inya Rd

YANGON

MYANMAR

+95 1-2305692

+95 1-2305693

+95 1-512699

+95 1-511035

Kuona Malo

Lolemba mpaka Lachisanu

7:30 a.m. mpaka 11:00 a.m. ndi 1:00 p.m. mpaka 3:00 p.m.

Nthawi yonse: Ola limodzi

Zimene Timachita

Timamasulira mabuku ofotokoza nkhani za m’Baibulo m’Chimyama, Chitchini (Hakha), Chikayini (Sgaw) ndiponso zinenero zina 10.

Koperani pepala losonyeza ofesi yathu.