Pitani ku nkhani yake

Mfundo Zokhudza Maofesi Ndiponso Kuona Malo

Tikukuitanani kuti mudzaone maofesi athu komanso malo athu osindikizira mabuku ndipo tidzakulandirani ndi manja awiri. Dziwani malo amene kuli maofesiwa komanso nthawi imene mungaone malo.

 

Moldova

Str Gr Ureche 75

MD-2005 CHISINAU

REPUBLIC OF MOLDOVA

+373 22-22-86-26

Kuona Malo

Lolemba mpaka Lachisanu

8:00 a.m. mpaka 11:00 a.m. ndi 1:00 p.m. mpaka 4:00 p.m.

Nthawi yonse: Ola limodzi

Zimene Timachita

Timayang’anira ntchito imene mipingo yoposa 20,000 ya Mboni za Yehova ikugwira. Mwezi uliwonse, timatumiza mabuku olemera matani oposa 16 kumipingo pafupifupi 250 ku Moldova.

Koperani pepala losonyeza ofesi yathu.