Pitani ku nkhani yake

Pitani ku menyu yachiwiri

Mboni za Yehova

Chichewa

Mfundo Zokhudza Maofesi Ndiponso Kuona Malo

Tikukuitanani kuti mudzaone maofesi athu komanso malo athu osindikizira mabuku ndipo tidzakulandirani ndi manja awiri. Dziwani malo amene kuli maofesiwa komanso nthawi imene mungaone malo.

 

Mexico

Ave Jardin No. 10

Fraccionamiento El Tejocote

56265 TEXCOCO, MEX

MEXICO

+52 555-133-3000

+52 555-133-3099

+52 555-858-0100

+52 555-858-0199

Kuona Malo

Lolemba mpaka Lachisanu

8:00 a.m. mpaka 11:00 a.m. ndi 1:00 p.m. mpaka 4:00 p.m.

Nthawi yonse: Maola awiri ndi hafu

Zimene Timachita

Timayang’anira ntchito yomasulira mabuku ofotokoza nkhani za m’Baibulo m’zinenero 49 za m’dera lonse la ku Mexico mpaka ku Panama. Timasindikiza mabuku m’zinenero zoposa 60 ndiponso timatumiza mabuku a zinenero zoposa 80 kumayiko oposa 10.

Koperani pepala losonyeza ofesi yathu.