Pitani ku nkhani yake

Mfundo Zokhudza Maofesi Ndiponso Kuona Malo

Tikukuitanani kuti mudzaone maofesi athu komanso malo athu osindikizira mabuku ndipo tidzakulandirani ndi manja awiri. Dziwani malo amene kuli maofesiwa komanso nthawi imene mungaone malo.

 

Malawi

Plot 38, Area 32

Paul Kagame Road

LILONGWE

MALAWI

+265 1-762-111

Kuona Malo

Lolemba mpaka Lachisanu

8:00 a.m. mpaka 11:00 a.m. ndi 1:00 p.m. mpaka 4:00 p.m.

Nthawi yonse: Ola limodzi ndi hafu

Zimene Timachita

Timamasulira mabuku ofotokoza nkhani za m’Baibulo m’Chichewa, Chitonga, Chitumbuka, Chiyao ndiponso Chinenero Chamanja cha ku Malawi. Timayang’aniranso ntchito imene mipingo ya Mboni za Yehova yokwana 1,300 ikugwira m’Malawi.

Koperani pepala losonyeza ofesi yathu.