Pitani ku nkhani yake

Pitani ku menyu yachiwiri

Mboni za Yehova

Chichewa

Mfundo Zokhudza Maofesi Ndiponso Kuona Malo

Tikukuitanani kuti mudzaone maofesi athu komanso malo athu osindikizira mabuku ndipo tidzakulandirani ndi manja awiri. Dziwani malo amene kuli maofesiwa komanso nthawi imene mungaone malo.

 

Madagascar

Vavolombelon’i Jehovah

Lot 1207 MC

Mandrosoa

105 IVATO

MADAGASCAR

+261 2022-44837

+261 3302-44837 (Foni Yam’manja)

Kuona Malo

Lolemba mpaka Lachisanu

7:30 a.m. mpaka 11:00 a.m. ndi 1:00 p.m. mpaka 4:00 p.m.

Nthawi yonse: Ola limodzi

Zimene Timachita

Timamasulira mabuku ofotokoza nkhani za m’Baibulo m’Chimalagase, Chitankarana, Chitanduroyi ndiponso Chivezo. Timajambula mavidiyo ndiponso zinthu zina zomvetsera m’Chimalagase. Timayang’aniranso ntchito imene mipingo pafupifupi 600 ya Mboni za Yehova ikugwira. Timatumiza mabuku oposa 270,000 komanso magazini oposa 600,000 mwezi uliwonse.

Koperani pepala losonyeza ofesi yathu.