Pitani ku nkhani yake

Mfundo Zokhudza Maofesi Ndiponso Kuona Malo

Tikukuitanani kuti mudzaone maofesi athu komanso malo athu osindikizira mabuku ndipo tidzakulandirani ndi manja awiri. Dziwani malo amene kuli maofesiwa komanso nthawi imene mungaone malo.

 

Liberia

Near Police Academy Junction

Kakata Highway

Paynesville City

MONROVIA

LIBERIA

+231 886-513-408

Kuona Malo

Lolemba mpaka Lachisanu

8:00 a.m. mpaka 11:00 a.m. ndi 1:30 p.m. mpaka 4:00 p.m

Nthawi yonse: Ola limodzi

Zimene Timachita

Timayang’anira ntchito yophunzitsa Baibulo imene Mboni za Yehova zoposa 5,500 zikugwira m’dziko lonse la Liberia.

Koperani pepala losonyeza ofesi yathu.