Pitani ku nkhani yake

Pitani ku menyu yachiwiri

Mboni za Yehova

Chichewa

Mfundo Zokhudza Maofesi Ndiponso Kuona Malo

Tikukuitanani kuti mudzaone maofesi athu komanso malo athu osindikizira mabuku ndipo tidzakulandirani ndi manja awiri. Dziwani malo amene kuli maofesiwa komanso nthawi imene mungaone malo.

 

Korea

Sindumangok-ro 73, Gongdo-eup

Anseong-si, Gyeonggi-do

REPUBLIC OF KOREA

+82 31-690-0033

Kuona Malo

Lolemba mpaka Lachisanu

8:00 a.m. mpaka 11:00 a.m. ndi 1:00 p.m. mpaka 4:00 p.m.

Nthawi yonse: Maola awiri

Zimene Timachita

Chaka chilichonse timasindikiza magazini 18 miliyoni m’zinenero 6 ndiponso timatumiza mabuku ndi magazini olemera matani 850. Timamasulira mabuku m’Chikoreya komanso m’Chinenero Chamanja cha ku Korea. Timajambulanso mavidiyo m’Chinenero Chamanja cha ku Korea.

Koperani pepala losonyeza ofesi yathu.