Pitani ku nkhani yake

Mfundo Zokhudza Maofesi Ndiponso Kuona Malo

Tikukuitanani kuti mudzaone maofesi athu komanso malo athu osindikizira mabuku ndipo tidzakulandirani ndi manja awiri. Dziwani malo amene kuli maofesiwa komanso nthawi imene mungaone malo.

 

Indonesia

Saksi Saksi Yehuwa Indonesia

Central Park APL Office Tower, Floor 31

Jl. S. Parman Kav. 28

Jakarta 11470

INDONESIA

+62-21-2986-0800

Kuona Malo

Lolemba mpaka Lachisanu

9:00 a.m. mpaka 11:00 a.m. ndi 1:30 p.m. mpaka 4:00 p.m.

Nthawi yonse: Ola limodzi ndi hafu

Zimene Timachita

Timamasulira mabuku a nkhani za m’Baibulo m’zinenero za ku Indonesia ndiponso m’zinenero zina 25. Timatumiza mabuku m’zilumba zosiyanasiyana za ku Indonesia.

Koperani pepala losonyeza ofesi yathu.