Pitani ku nkhani yake

Mfundo Zokhudza Maofesi Ndiponso Kuona Malo

Tikukuitanani kuti mudzaone maofesi athu komanso malo athu osindikizira mabuku ndipo tidzakulandirani ndi manja awiri. Dziwani malo amene kuli maofesiwa komanso nthawi imene mungaone malo.

 

India

927/1 Addevishwanathapura

Rajanukunte

Yelahanka

BANGALORE-KAR 560 064

INDIA

+91 98-4547-6425

+91 98-4534-8815

+91 96-8611-4293

+91 80-2846-8072

+91 80-2846-8073

Kuona Malo

Lolemba mpaka Lachisanu

8:00 a.m. mpaka 11:00 a.m. ndi 1:00 p.m. mpaka 3:00 p.m.

Nthawi yonse: Ola limodzi ndi hafu

Zimene Timachita

Timamasulira mabuku ofotokoza nkhani za m’Baibulo m’zinenero 18 za ku India. Timasindikiza mabuku m’zinenero 24 za ku India. Timatumiza mabuku m’dziko lonse la India komanso m’mayiko ena 9.

Koperani pepala losonyeza ofesi yathu.