Pitani ku nkhani yake

Mfundo Zokhudza Maofesi Ndiponso Kuona Malo

Tikukuitanani kuti mudzaone maofesi athu komanso malo athu osindikizira mabuku ndipo tidzakulandirani ndi manja awiri. Dziwani malo amene kuli maofesiwa komanso nthawi imene mungaone malo.

 

Hungary

BUDAPEST

Kövirózsa u. 1.

H-1163

HUNGARY

+361 401-1100

Kuona Malo

Lolemba mpaka Lachisanu

9:00 a.m., 10:30 a.m., 2:00 p.m. ndi 3:30 p.m.

Nthawi yonse: Ola limodzi ndi mphindi 15

Zimene Timachita

Timayang’anira ntchito imene mipingo yoposa ??? ya Mboni za Yehova ikugwira ku Hungary ndiponso timathandiza mipingo ya Chihangare ku Slovakia ndi Ukraine. Timamasulira mabuku ofotokoza nkhani za m’Baibulo m’Chihangare ndi m’Chilovari. Timajambula zinthu zina zomvetsera m’Chihangare ndiponso mavidiyo a Chinenero Chamanja cha ku Hangary.

Koperani pepala losonyeza ofesi yathu.