Pitani ku nkhani yake

Mfundo Zokhudza Maofesi Ndiponso Kuona Malo

Tikukuitanani kuti mudzaone maofesi athu komanso malo athu osindikizira mabuku ndipo tidzakulandirani ndi manja awiri. Dziwani malo amene kuli maofesiwa komanso nthawi imene mungaone malo.

 

Hong Kong

Watch Tower Bible and Tract Society

19/F, 1 Hung To Road,

Kwun Tong,

KOWLOON, HONG KONG

+852 2337-1686

Kuona Malo

Lolemba mpaka Lachisanu

8:15 a.m. mpaka 11:00 a.m. ndi 1:00 p.m. mpaka 4:00 p.m.

Nthawi yonse: Mphindi 45

Zimene Timachita

Timamasulira mabuku ofotokoza nkhani za m’Baibulo m’Chitchainizi (Chenicheni), Chitchainizi (Chosavuta) Chipijini ndiponso Chiwiguri (cha ku Arabia). Timajambulanso zinthu zina zomvetsera m’Chitchainizi (Chikantonizi) ndiponso mavidiyo m’Chinenero Chamanja cha ku China.

Koperani pepala losonyeza ofesi yathu.