Pitani ku nkhani yake

Pitani ku menyu yachiwiri

Mboni za Yehova

Chichewa

Mfundo Zokhudza Maofesi Ndiponso Kuona Malo

Tikukuitanani kuti mudzaone maofesi athu komanso malo athu osindikizira mabuku ndipo tidzakulandirani ndi manja awiri. Dziwani malo amene kuli maofesiwa komanso nthawi imene mungaone malo.

 

Guam

Watch Tower Bible and Tract Society

143 Jehovah St

BARRIGADA GU 96913

+1 671-632-0429

Kuona Malo

Lolemba mpaka Lachisanu

8:00 a.m. mpaka 11:00 a.m. ndi 1:00 p.m. mpaka 4:00 p.m.

Nthawi yonse: Ola limodzi

Zimene Timachita

Timamasulira mabuku ofotokoza nkhani za m’Baibulo m’zinenero 6 za pazilumba zosiyanasiyana zapanyanja ya Pacific. Zinenerozi ndi Chichukizi, Chikosireya, Chimasho, Chipalau, Chiponape ndi Chiyapizi.

Koperani pepala losonyeza ofesi yathu.