Pitani ku nkhani yake

Pitani ku menyu yachiwiri

Mboni za Yehova

Chichewa

Mfundo Zokhudza Maofesi Ndiponso Kuona Malo

Tikukuitanani kuti mudzaone maofesi athu komanso malo athu osindikizira mabuku ndipo tidzakulandirani ndi manja awiri. Dziwani malo amene kuli maofesiwa komanso nthawi imene mungaone malo.

 

Greece

Watch Tower Bible and Tract Society

Kifisias 77

GR 151 24 MAROUSI

GREECE

+30 210-619-7630

Kuona Malo

Lolemba mpaka Lachisanu

8:00 a.m. mpaka 11:00 a.m. ndi 1:00 p.m. mpaka 4:00 p.m.

Nthawi yonse: Ola limodzi

Zimene Timachita

Timamasulira mabuku ofotokoza nkhani za m’Baibulo m’Chigiriki, Chiromane cha ku Greece komanso Chinenero Chamanja cha ku Greece. Timayang’aniranso ntchito imene Mboni za Yehova zikugwira ku Greece ndi ku Cyprus.

Koperani pepala losonyeza ofesi yathu.