Pitani ku nkhani yake

Pitani ku menyu yachiwiri

Mboni za Yehova

Chichewa

Mfundo Zokhudza Maofesi Ndiponso Kuona Malo

Tikukuitanani kuti mudzaone maofesi athu komanso malo athu osindikizira mabuku ndipo tidzakulandirani ndi manja awiri. Dziwani malo amene kuli maofesiwa komanso nthawi imene mungaone malo.

 

Germany

Jehovas Zeugen

Am Steinfels

65618 SELTERS

GERMANY

+49 6483-41-0

Kuona Malo

Lolemba mpaka Lachisanu

8:00 a.m. mpaka 11:00 a.m. ndi 1:00 p.m. mpaka 4:00 p.m.

Nthawi yonse: Maola awiri

Zimene Timachita

Timasindikiza mabuku 17 miliyoni ndiponso magazini 165 miliyoni chaka chilichonse. Timatumiza mabuku ndi magazini olemera matani 11,000 komanso m’zinenero 280 chaka chilichonse, m’mayiko 40.

Koperani pepala losonyeza ofesi yathu.